Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iwo alola ena mwa ana aakazi a mitundu inayo kuti akhale akazi awo ndi akazi a ana awo aamuna,+ ndipo iwo omwe ndi mtundu wopatulika,+ asakanikirana+ ndi anthu a mitundu ina. Akalonga ndi atsogoleri ndiwo ali patsogolo+ pa kusakhulupirika kumeneku.”

  • Salimo 38:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Pakuti zolakwa zanga zakwera kupitirira mutu wanga.+

      Zandilemera kwambiri ngati katundu wolemera.+

  • Salimo 106:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Tachimwa mofanana ndi makolo athu.+

      Tachita zinthu zosayenera, tachita zinthu zoipa.+

  • Yesaya 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Yehova akuti, “Bwerani tsopano anthu inu. Tiyeni tikambirane ndipo ine ndikuthandizani kuti mukhalenso pa ubwenzi wabwino ndi ine.+ Ngakhale machimo anu atakhala ofiira kwambiri, adzayera kwambiri.+ Ngakhale atakhala ofiira ngati magazi, adzayera ngati thonje.

  • Yesaya 59:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pakuti zolakwa zathu zachuluka pamaso panu,+ ndipo tchimo lathu lililonse likupereka umboni wotsutsana nafe.+ Pakuti zolakwa zathu zili pa ife, ndipo zochimwa zathu tikuzidziwa bwino.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena