Ezara 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinayamba kunena kuti:+ “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi+ kuti ndikweze nkhope yanga kwa inuyo Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu+ zachuluka pamutu pathu ndipo machimo athu achuluka kwambiri mpaka kufika kumwamba.+ Salimo 40:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti masoka anandizungulira moti sindinathe kuwawerenga.+Zolakwa zanga zochuluka zinandifikira modzidzimutsa moti sindinathe kuziona mmene zinachulukira.+Zinachuluka kwambiri kuposa tsitsi la kumutu kwanga,+Ndipo ndinataya mtima.+
6 Kenako ndinayamba kunena kuti:+ “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi+ kuti ndikweze nkhope yanga kwa inuyo Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu+ zachuluka pamutu pathu ndipo machimo athu achuluka kwambiri mpaka kufika kumwamba.+
12 Pakuti masoka anandizungulira moti sindinathe kuwawerenga.+Zolakwa zanga zochuluka zinandifikira modzidzimutsa moti sindinathe kuziona mmene zinachulukira.+Zinachuluka kwambiri kuposa tsitsi la kumutu kwanga,+Ndipo ndinataya mtima.+