2 Mbiri 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nthawi ndi nthawi ankapereka nsembe+ ndi kufukiza nsembe yautsi pamalo okwezeka,+ pamapiri,+ ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.+
4 Nthawi ndi nthawi ankapereka nsembe+ ndi kufukiza nsembe yautsi pamalo okwezeka,+ pamapiri,+ ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.+