2 Mafumu 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Hezekiya anali ndi zaka 25 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 29. Mayi ake dzina lawo linali Abi mwana wa Zekariya.+
2 Hezekiya anali ndi zaka 25 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 29. Mayi ake dzina lawo linali Abi mwana wa Zekariya.+