1 Mbiri 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa ana a Merari+ panali Asaya+ mtsogoleri wawo ndi abale ake okwanira 220. 1 Mbiri 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana a Merari+ anali Mali ndi Musi.+ Ana a Mali anali Eleazara+ ndi Kisi.