1 Mbiri 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nyadirani dzina+ lake loyera.+Mtima wa anthu ofunafuna Yehova usangalale.+ Salimo 92:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti mwandichititsa kusangalala, inu Yehova, chifukwa cha zochita zanu.Ndimafuula mosangalala chifukwa cha ntchito ya manja anu.+
4 Pakuti mwandichititsa kusangalala, inu Yehova, chifukwa cha zochita zanu.Ndimafuula mosangalala chifukwa cha ntchito ya manja anu.+