Deuteronomo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mudzawononge+ malo onse amene ali pamapiri ataliatali, pazitunda ndi pansi pa mitengo ikuluikulu ya masamba obiriwira, pamene mitundu imene mukukailanda dziko lawo imatumikirirapo milungu yawo.+
2 Mudzawononge+ malo onse amene ali pamapiri ataliatali, pazitunda ndi pansi pa mitengo ikuluikulu ya masamba obiriwira, pamene mitundu imene mukukailanda dziko lawo imatumikirirapo milungu yawo.+