Ezara 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atamandike Yehova Mulungu wa makolo athu,+ amene waika maganizo amenewa mumtima+ mwa mfumu, kuti nyumba ya Yehova imene ili ku Yerusalemu ikongoletsedwe.+
27 Atamandike Yehova Mulungu wa makolo athu,+ amene waika maganizo amenewa mumtima+ mwa mfumu, kuti nyumba ya Yehova imene ili ku Yerusalemu ikongoletsedwe.+