2 Mbiri 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ana a Isiraeli ndi Yuda amene anali kukhala m’mizinda ya Yuda+ anabweretsa chakhumi cha ng’ombe, nkhosa, ndi chakhumi cha zinthu zopatulika+ zimene anaziyeretsera Yehova Mulungu wawo. Anabweretsa zinthu zimenezi zambiri mpaka kukwana milumilu.
6 Ana a Isiraeli ndi Yuda amene anali kukhala m’mizinda ya Yuda+ anabweretsa chakhumi cha ng’ombe, nkhosa, ndi chakhumi cha zinthu zopatulika+ zimene anaziyeretsera Yehova Mulungu wawo. Anabweretsa zinthu zimenezi zambiri mpaka kukwana milumilu.