2 Mbiri 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iwo anasonkhanitsa abale awo pamodzi n’kudziyeretsa.+ Ndiyeno anabwera kudzayeretsa+ nyumba ya Yehova mogwirizana ndi lamulo la mfumu potsatira mawu+ a Yehova.
15 Iwo anasonkhanitsa abale awo pamodzi n’kudziyeretsa.+ Ndiyeno anabwera kudzayeretsa+ nyumba ya Yehova mogwirizana ndi lamulo la mfumu potsatira mawu+ a Yehova.