Salimo 76:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu olimba mtima alandidwa zinthu zawo,+Iwo awodzera ndi kugona tulo,+Ndipo palibe ngakhale mmodzi mwa anthu onse olimba mtimawo amene ali ndi mphamvu zotsutsa.+
5 Anthu olimba mtima alandidwa zinthu zawo,+Iwo awodzera ndi kugona tulo,+Ndipo palibe ngakhale mmodzi mwa anthu onse olimba mtimawo amene ali ndi mphamvu zotsutsa.+