Yesaya 46:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Tamverani inu anthu osamva,+ inu anthu amene muli kutali ndi chilungamo.+ Luka 1:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Wachita zamphamvu ndi dzanja lake,+ wabalalitsira kutali odzikweza m’zolinga za mitima yawo.+