Salimo 119:150 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 150 Okonda kuchita khalidwe lotayirira+ abwera pafupi ndi ine.Iwo atalikirana kwambiri ndi chilamulo chanu.+ Yeremiya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Kodi makolo anu anandipeza ndi chiyani chosalungama+ kuti akhale patali ndi ine?+ Anandipeza ndi chiyani kuti ayambe kutsatira fano lopanda pake+ iwonso n’kukhala anthu opanda pake?+
150 Okonda kuchita khalidwe lotayirira+ abwera pafupi ndi ine.Iwo atalikirana kwambiri ndi chilamulo chanu.+
5 Yehova wanena kuti: “Kodi makolo anu anandipeza ndi chiyani chosalungama+ kuti akhale patali ndi ine?+ Anandipeza ndi chiyani kuti ayambe kutsatira fano lopanda pake+ iwonso n’kukhala anthu opanda pake?+