Yesaya 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 N’chiyaninso chimene ndingachite m’munda wanga wa mpesawu chimene sindinachitemo kale?+ Ine ndinali kuyembekezera kuti ubereka mphesa zabwino, koma n’chifukwa chiyani unabereka mphesa zam’tchire? Mika 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Inu anthu anga,+ ndakulakwirani chiyani? Kodi ndakutopetsani mwa njira yanji?+ Perekani umboni wonditsutsa.+
4 N’chiyaninso chimene ndingachite m’munda wanga wa mpesawu chimene sindinachitemo kale?+ Ine ndinali kuyembekezera kuti ubereka mphesa zabwino, koma n’chifukwa chiyani unabereka mphesa zam’tchire?
3 “Inu anthu anga,+ ndakulakwirani chiyani? Kodi ndakutopetsani mwa njira yanji?+ Perekani umboni wonditsutsa.+