Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iwo andichititsa nsanje ndi milungu yachabe.+

      Andisautsa ndi mafano awo opanda pake.+

      Ndipo ine ndidzawachititsa nsanje ndi anthu achabe,+

      Ndidzawakhumudwitsa ndi mtundu wopusa.+

  • 1 Mafumu 16:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Iye anali kuyenda m’njira zonse za Yerobowamu mwana wa Nebati,+ ndi m’tchimo lake limene anachimwitsa nalo Isiraeli mwa kukwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mafano awo opanda pake.+

  • 2 Mafumu 17:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Iwo anapitiriza kukana malamulo ndi pangano+ limene iye anapangana ndi makolo awo, ndiponso zikumbutso+ zimene iye anali kuwachenjeza nazo. M’malomwake anayamba kutsatira mafano opanda pake+ ndipo iwowo nawonso anakhala opanda pake.+ Anatsatira mitundu imene inawazungulira, imene Yehova anawalamula kuti asamachite zofanana nayo.+

  • Machitidwe 14:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 kuti: “Anthu inu, mukuchitiranji zimenezi? Ifenso ndife anthu+ okhala ndi zofooka+ ngati inu nomwe, ndipo tikulengeza uthenga wabwino kwa inu. Tikuchita izi kuti musiye zachabechabe zimenezi+ ndi kutembenukira kwa Mulungu wamoyo,+ amene anapanga kumwamba,+ dziko lapansi, nyanja ndi zonse zokhala mmenemo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena