Deuteronomo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova Mulungu wathu anachita nafe pangano ku Horebe.+ Deuteronomo 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 kuti muchite pangano+ ndi Yehova Mulungu wanu mwa kulumbira, pangano limene Yehova Mulungu wanu akuchita nanu lero.+
12 kuti muchite pangano+ ndi Yehova Mulungu wanu mwa kulumbira, pangano limene Yehova Mulungu wanu akuchita nanu lero.+