Deuteronomo 32:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo andichititsa nsanje ndi milungu yachabe.+Andisautsa ndi mafano awo opanda pake.+Ndipo ine ndidzawachititsa nsanje ndi anthu achabe,+Ndidzawakhumudwitsa ndi mtundu wopusa.+ 1 Samueli 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musapatuke kuti mutsatire milungu yopanda pake,+ yopanda phindu,+ imene singakulanditseni, pakuti ndi yopanda pake. Yeremiya 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iwo ndi achabechabe, ntchito yoyenera kutonzedwa.+ Mulungu akadzatembenukira kwa iwo, adzawawononga.+ 1 Akorinto 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+
21 Iwo andichititsa nsanje ndi milungu yachabe.+Andisautsa ndi mafano awo opanda pake.+Ndipo ine ndidzawachititsa nsanje ndi anthu achabe,+Ndidzawakhumudwitsa ndi mtundu wopusa.+
21 Musapatuke kuti mutsatire milungu yopanda pake,+ yopanda phindu,+ imene singakulanditseni, pakuti ndi yopanda pake.
15 Iwo ndi achabechabe, ntchito yoyenera kutonzedwa.+ Mulungu akadzatembenukira kwa iwo, adzawawononga.+
4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+