Miyambo 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova adzagwetsa nyumba za anthu odzikuza,+ koma adzakhazikitsa malire a malo a mkazi wamasiye.+