Salimo 52:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu adzakupasula kosatha.+Adzakugwetsa ndi kukukokera kunja kwa hema wako,+Ndipo adzakuzula ndithu m’dziko la anthu amoyo.+ [Seʹlah.] Luka 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndithu ndikukuuzani, Munthu ameneyu anapita kwawo ataonedwa kukhala wolungama kwambiri+ kusiyana ndi wina uja, chifukwa aliyense wodzikweza adzam’nyazitsa, koma wodzichepetsa adzamukweza.”+
5 Mulungu adzakupasula kosatha.+Adzakugwetsa ndi kukukokera kunja kwa hema wako,+Ndipo adzakuzula ndithu m’dziko la anthu amoyo.+ [Seʹlah.]
14 Ndithu ndikukuuzani, Munthu ameneyu anapita kwawo ataonedwa kukhala wolungama kwambiri+ kusiyana ndi wina uja, chifukwa aliyense wodzikweza adzam’nyazitsa, koma wodzichepetsa adzamukweza.”+