Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 16:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndiyeno Delila anati: “Afilisiti aja abwera Samisoni!” Pamenepo Samisoni anagalamuka ku tulo take ndi kunena kuti: “Ndituluka monga mwa masiku onse+ kukalimbana nawo.” Koma iye sanadziwe kuti Yehova anali atam’chokera.+

  • 1 Akorinto 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Palibe mayesero amene mwakumana nawo osiyana ndi amene amagwera anthu ena.+ Koma Mulungu ndi wokhulupirika+ ndipo sadzalola kuti muyesedwe kufika pamene simungapirire,+ koma pamene mukukumana ndi mayeserowo iye adzapereka njira yopulumukira+ kuti muthe kuwapirira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena