2 Mafumu 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Manase anatentha* mwana wake wamwamuna pamoto,+ ndipo ankachita zamatsenga,+ ankawombeza,*+ ndiponso anaika anthu olankhula ndi mizimu ndi olosera+ zam’tsogolo. Iye anachita zinthu zambiri zoipa pamaso pa Yehova ndiponso zomukwiyitsa.
6 Manase anatentha* mwana wake wamwamuna pamoto,+ ndipo ankachita zamatsenga,+ ankawombeza,*+ ndiponso anaika anthu olankhula ndi mizimu ndi olosera+ zam’tsogolo. Iye anachita zinthu zambiri zoipa pamaso pa Yehova ndiponso zomukwiyitsa.