Nehemiya 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana aamuna a Haseneya anamanga Chipata cha Nsomba.+ Iwo anachipangira felemu lamatabwa+ ndi kuika zitseko zake,+ akapichi ake ndi mipiringidzo yake.+
3 Ana aamuna a Haseneya anamanga Chipata cha Nsomba.+ Iwo anachipangira felemu lamatabwa+ ndi kuika zitseko zake,+ akapichi ake ndi mipiringidzo yake.+