-
2 Mbiri 27:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Yotamu anamenyana ndi mfumu ya ana a Amoni+ ndipo pomalizira pake anawaposa mphamvu. Choncho chaka chimenecho ana a Amoni anam’patsa matalente a siliva* 100 ndi tirigu+ wokwana miyezo 10,000 ya kori,*+ komanso balere wokwana miyezo 10,000 ya kori.+ Izi n’zimene ana a Amoni anamulipira. Anamulipiranso zomwezi m’chaka chachiwiri ndi chachitatu.+
-