2 Mafumu 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova anakhala naye,+ ndipo kulikonse kumene ankapita anali kuchita zinthu mwanzeru.+ Anapandukira mfumu ya Asuri n’kukana kuitumikira.+ Miyambo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuopa anthu n’kumene kumatchera msampha,+ koma wokhulupirira Yehova adzatetezedwa.+ Luka 14:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma akaona kuti sangakwanitse, mwamsanga amatumiza akazembe kwa mfumu inayo isanafike pafupi, kukapempha mtendere.+
7 Yehova anakhala naye,+ ndipo kulikonse kumene ankapita anali kuchita zinthu mwanzeru.+ Anapandukira mfumu ya Asuri n’kukana kuitumikira.+
32 Koma akaona kuti sangakwanitse, mwamsanga amatumiza akazembe kwa mfumu inayo isanafike pafupi, kukapempha mtendere.+