1 Samueli 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide anali kuchita zinthu mwanzeru+ nthawi zonse m’njira zake zonse, ndipo Yehova anali naye.+ Miyambo 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+
18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+