2 Mafumu 23:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Yehoyakimu anali ndi zaka 25+ pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Ruma, ndipo dzina lawo linali Zebida mwana wa Pedaya.
36 Yehoyakimu anali ndi zaka 25+ pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Ruma, ndipo dzina lawo linali Zebida mwana wa Pedaya.