3 Mawuwo anapitiriza kufika kwa Yeremiya m’masiku a Yehoyakimu+ mfumu ya Yuda, mwana wa Yosiya, mpaka m’chaka cha 11, kumapeto kwa ulamuliro wa Zedekiya+ mfumu ya Yuda, mwana wa Yosiya, pamene anthu a mu Yerusalemu anatengedwa kupita ku ukapolo m’mwezi wachisanu.+