2 Mafumu 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komanso mfumu ya Babulo+ inatenga Mataniya, bambo ake aang’ono+ a Yehoyakini, n’kuwaika kukhala mfumu m’malo mwake. Kenako inam’sintha dzina Mataniya kuti akhale Zedekiya.+ 2 Mbiri 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zedekiya+ anali ndi zaka 21 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+
17 Komanso mfumu ya Babulo+ inatenga Mataniya, bambo ake aang’ono+ a Yehoyakini, n’kuwaika kukhala mfumu m’malo mwake. Kenako inam’sintha dzina Mataniya kuti akhale Zedekiya.+