2 Mafumu 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zedekiya+ anali ndi zaka 21 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Libina, ndipo dzina lawo linali Hamutali+ mwana wa Yeremiya. 2 Mbiri 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zedekiya+ anali ndi zaka 21 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Yeremiya 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anauza Yeremiya mawu,+ pamene Mfumu Zedekiya+ inatumiza Pasuri+ mwana wa Malikiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya, wansembe, ndi uthenga wakuti: Yeremiya 39:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’chaka cha 11 cha ulamuliro wa Zedekiya, m’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9, anaboola mpanda wa mzindawo.+
18 Zedekiya+ anali ndi zaka 21 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Libina, ndipo dzina lawo linali Hamutali+ mwana wa Yeremiya.
21 Yehova anauza Yeremiya mawu,+ pamene Mfumu Zedekiya+ inatumiza Pasuri+ mwana wa Malikiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya, wansembe, ndi uthenga wakuti:
2 M’chaka cha 11 cha ulamuliro wa Zedekiya, m’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9, anaboola mpanda wa mzindawo.+