2 Mafumu 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komanso mfumu ya Babulo+ inatenga Mataniya, bambo ake aang’ono+ a Yehoyakini, n’kuwaika kukhala mfumu m’malo mwake. Kenako inam’sintha dzina Mataniya kuti akhale Zedekiya.+
17 Komanso mfumu ya Babulo+ inatenga Mataniya, bambo ake aang’ono+ a Yehoyakini, n’kuwaika kukhala mfumu m’malo mwake. Kenako inam’sintha dzina Mataniya kuti akhale Zedekiya.+