1 Mbiri 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Golide, siliva, mkuwa, ndi zitsulo n’zosatheka kuziwerenga.+ Yamba kugwira ntchito imeneyi,+ ndipo Yehova akhale nawe.”+ Zekariya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Fulumira Ziyoni!+ Thawa, iwe amene ukukhala ndi mwana wamkazi wa Babulo.+
16 Golide, siliva, mkuwa, ndi zitsulo n’zosatheka kuziwerenga.+ Yamba kugwira ntchito imeneyi,+ ndipo Yehova akhale nawe.”+