2 Mbiri 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Solomo mwana wa Davide anapitiriza kukhala wamphamvu mu ufumu wake.+ Yehova Mulungu wake anali naye,+ ndipo anapitiriza kumukulitsa kuposa wina aliyense.+ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
1 Solomo mwana wa Davide anapitiriza kukhala wamphamvu mu ufumu wake.+ Yehova Mulungu wake anali naye,+ ndipo anapitiriza kumukulitsa kuposa wina aliyense.+
31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+