1 Mafumu 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mtumiki wanune ndili pakati pa anthu anu amene mwawasankha,+ anthu ochuluka zedi amene sangatheke kuwerengeka chifukwa chochuluka.+ Salimo 72:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aweruzire anthu milandu mwachilungamo,+Ndipo aweruze milandu ya osautsika ndi ziweruzo zolungama.+
8 Mtumiki wanune ndili pakati pa anthu anu amene mwawasankha,+ anthu ochuluka zedi amene sangatheke kuwerengeka chifukwa chochuluka.+