Salimo 106:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Tipulumutseni inu Yehova Mulungu wathu,+Tisonkhanitseni pamodzi kuchokera m’mitundu ina,+Kuti titamande dzina lanu loyera,+Ndi kuti tilankhule mokondwa pokutamandani.+
47 Tipulumutseni inu Yehova Mulungu wathu,+Tisonkhanitseni pamodzi kuchokera m’mitundu ina,+Kuti titamande dzina lanu loyera,+Ndi kuti tilankhule mokondwa pokutamandani.+