1 Mafumu 8:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Mfumuyo ndi Aisiraeli onse amene anali nayo anayamba kupereka nsembe yaikulu pamaso pa Yehova.+