1 Mbiri 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chiwerengero chawo, pamodzi ndi abale awo ophunzitsidwa kuimbira Yehova,+ onse akatswiri,+ chinakwana 288.
7 Chiwerengero chawo, pamodzi ndi abale awo ophunzitsidwa kuimbira Yehova,+ onse akatswiri,+ chinakwana 288.