Deuteronomo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 koma mudzafunefune malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe pakati pa mafuko anu onse kuti aikepo dzina lake, kuti lizikhala pamenepo. Amenewo ndiwo malo amene muzidzapitako.+ Salimo 78:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Koma anasankha fuko la Yuda,+Phiri la Ziyoni limene analikonda.+
5 koma mudzafunefune malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe pakati pa mafuko anu onse kuti aikepo dzina lake, kuti lizikhala pamenepo. Amenewo ndiwo malo amene muzidzapitako.+