2 Mbiri 6:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 inuyo mumve muli kumwamba, malo anu okhala okhazikika.+ Mumve pemphero lawo ndi pempho lawo lopempha chifundo,+ ndipo muwachitire chilungamo.+ Mukhululukire+ anthu anu amene akuchimwirani. Salimo 103:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamanda amene akukukhululukira zolakwa zako zonse,+Iye amene akukuchiritsa matenda ako onse.+
39 inuyo mumve muli kumwamba, malo anu okhala okhazikika.+ Mumve pemphero lawo ndi pempho lawo lopempha chifundo,+ ndipo muwachitire chilungamo.+ Mukhululukire+ anthu anu amene akuchimwirani.