Levitiko 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Pa tsiku la 15 m’mwezi umenewu, muzichita chikondwerero cha Yehova cha mikate yopanda chofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda chofufumitsa imeneyi masiku 7.+
6 “‘Pa tsiku la 15 m’mwezi umenewu, muzichita chikondwerero cha Yehova cha mikate yopanda chofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda chofufumitsa imeneyi masiku 7.+