1 Mafumu 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa nthawi imeneyo, Hiramu anatumiza kwa mfumuyo golide wokwana matalente* 120.+ Salimo 72:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mafumu a ku Tarisi ndi m’zilumba+Adzapereka msonkho.+Mafumu a ku Sheba ndi SebaAdzapereka mphatso.+
10 Mafumu a ku Tarisi ndi m’zilumba+Adzapereka msonkho.+Mafumu a ku Sheba ndi SebaAdzapereka mphatso.+