Salimo 72:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mafumu a ku Tarisi ndi m’zilumba+Adzapereka msonkho.+Mafumu a ku Sheba ndi SebaAdzapereka mphatso.+ Yeremiya 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 mafumu onse a Aluya,+ mafumu onse a anthu a mitundu yosiyanasiyana amene amakhala m’chipululu,
10 Mafumu a ku Tarisi ndi m’zilumba+Adzapereka msonkho.+Mafumu a ku Sheba ndi SebaAdzapereka mphatso.+