1 Mafumu 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Bambo anu anaumitsa goli lathu. Tsopano inuyo mufewetse+ ntchito yowawa ya bambo anu ndi goli lawo lolemera+ limene anatisenzetsa, ndipo tidzakutumikirani.”+
4 “Bambo anu anaumitsa goli lathu. Tsopano inuyo mufewetse+ ntchito yowawa ya bambo anu ndi goli lawo lolemera+ limene anatisenzetsa, ndipo tidzakutumikirani.”+