1 Mafumu 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pa nthawi imeneyo, Yerobowamu anatuluka mu Yerusalemu, ndipo Ahiya+ Msilo+ yemwe anali mneneri, anam’peza panjira. Ahiya anali atavala chovala chatsopano. Awiriwo anali okhaokha kumeneko.
29 Pa nthawi imeneyo, Yerobowamu anatuluka mu Yerusalemu, ndipo Ahiya+ Msilo+ yemwe anali mneneri, anam’peza panjira. Ahiya anali atavala chovala chatsopano. Awiriwo anali okhaokha kumeneko.