2 Mbiri 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amenewa ndiwo anali kutumikira mfumu, kuwonjezera pa anthu amene mfumuyo inawaika m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri+ m’dziko lonse la Yuda.
19 Amenewa ndiwo anali kutumikira mfumu, kuwonjezera pa anthu amene mfumuyo inawaika m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri+ m’dziko lonse la Yuda.