Yesaya 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu Yehova Mulungu wathu, ife takhalapo m’manja mwa ambuye ena kupatula inu.+ Koma chifukwa cha thandizo lanu, timatha kutchula dzina lanu.+
13 Inu Yehova Mulungu wathu, ife takhalapo m’manja mwa ambuye ena kupatula inu.+ Koma chifukwa cha thandizo lanu, timatha kutchula dzina lanu.+