2 Mbiri 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma iwo akhala atumiki ake+ kuti adziwe kusiyana kokhala atumiki anga+ ndi kokhala atumiki a maufumu a m’dzikoli.”+
8 Koma iwo akhala atumiki ake+ kuti adziwe kusiyana kokhala atumiki anga+ ndi kokhala atumiki a maufumu a m’dzikoli.”+