Ezara 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mum’patse ngakhale matalente* 100+ a siliva, tirigu wokwana miyezo 100 ya kori,*+ vinyo+ wokwana mitsuko*+ 100, mafuta okwana mitsuko 100,+ ndi mchere+ wochuluka.
22 Mum’patse ngakhale matalente* 100+ a siliva, tirigu wokwana miyezo 100 ya kori,*+ vinyo+ wokwana mitsuko*+ 100, mafuta okwana mitsuko 100,+ ndi mchere+ wochuluka.