Ekisodo 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Koma iwe, ulamule ana a Isiraeli kuti akupezere mafuta ounikira oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale ziziyaka nthawi zonse.+ Levitiko 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yambewu+ kwa Yehova, nsembe yakeyo izikhala ufa wosalala.+ Azithira mafuta ndi kuika lubani* pa ufawo.
20 “Koma iwe, ulamule ana a Isiraeli kuti akupezere mafuta ounikira oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale ziziyaka nthawi zonse.+
2 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yambewu+ kwa Yehova, nsembe yakeyo izikhala ufa wosalala.+ Azithira mafuta ndi kuika lubani* pa ufawo.