Genesis 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zidzatero chifukwa Abulahamu anamvera mawu anga, ndipo anachita zofuna zanga ndi kusunga malamulo anga onse.”+ Numeri 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngakhale mtambowo ukhale masiku ambiri pamwamba pa chihema, ana a Isiraeli ankamverabe Yehova, ndipo sankachoka pamalopo.+ Deuteronomo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Nthawi zonse uzikonda Yehova Mulungu wako+ ndi kuchita zofuna zake, kutsatira mfundo zake, zigamulo zake+ ndi malamulo ake.
5 Zidzatero chifukwa Abulahamu anamvera mawu anga, ndipo anachita zofuna zanga ndi kusunga malamulo anga onse.”+
19 Ngakhale mtambowo ukhale masiku ambiri pamwamba pa chihema, ana a Isiraeli ankamverabe Yehova, ndipo sankachoka pamalopo.+
11 “Nthawi zonse uzikonda Yehova Mulungu wako+ ndi kuchita zofuna zake, kutsatira mfundo zake, zigamulo zake+ ndi malamulo ake.