2 Mbiri 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chotero ufumu wa Yehosafati unalibe chosokoneza chilichonse, ndipo Mulungu wake anapitiriza kumupatsa mpumulo pakati pa adani ake onse omuzungulira.+ Miyambo 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Olungama akachuluka, anthu amasangalala,+ koma aliyense woipa akayamba kulamulira, anthu amabuula.+
30 Chotero ufumu wa Yehosafati unalibe chosokoneza chilichonse, ndipo Mulungu wake anapitiriza kumupatsa mpumulo pakati pa adani ake onse omuzungulira.+
2 Olungama akachuluka, anthu amasangalala,+ koma aliyense woipa akayamba kulamulira, anthu amabuula.+